Deuteronomo 29:6 BL92

6 Simunadya mkate, simunamwa vinyo kapena cakumwa colimba; kuti mudziwe kuti Ine ndine Yehova Mulungu wanu.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 29

Onani Deuteronomo 29:6 nkhani