12 Silikhala m'mwamba, kuti mukati, Adzatikwerera m'mwamba ndani, ndi kubwera nalo kwa ife, ndi kutimvetsa ili, kuti tilicite?
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 30
Onani Deuteronomo 30:12 nkhani