15 Koma Yesuruni anasanduka wonenepa, natazira;Wasanduka wonenepa, wakula, wakuta ndi mafuta;Pamenepo anasiya Mulungu amene anamlenga,Napeputsa thanthwe la cipulumutso cace.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 32
Onani Deuteronomo 32:15 nkhani