21 Anautsa nsanje yanga ndi cinthu cosati Mulungu;Anautsa mkwiyo wanga om zopanda pace zao.Ndidzautsa nsanje yao ndi iwo osakhala mtundu wa anthu;Ndidzautsa mkwiyo wao ndi mtundu wa anthu opusa.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 32
Onani Deuteronomo 32:21 nkhani