Deuteronomo 33:13 BL92

13 Ndipo za Yosefe anati,Yehova adalitse dziko lace;Ndi zinthu zofunikatu za m'mwamba, ndi mame,Ndi madzi okhala pansipo;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 33

Onani Deuteronomo 33:13 nkhani