12 Za Benjamini anati,Wokondedwa wa Yehova adzakhala ndi iye mokhazikika;Amphimba tsiku lonse,Inde akhalitsa pakati pa mapewa ace.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 33
Onani Deuteronomo 33:12 nkhani