11 Dalitsani, Yehova, mphamvu yace,Nimulandire nchito ya manja ace;Akantheni m'cuuno iwo akumuukira,Ndi iwo akumuda, kuti asaukenso.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 33
Onani Deuteronomo 33:11 nkhani