10 Adzaphunzitsa Yakobo maweruzo anu,Ndi Israyeli cilamulo canu;Adzaika cofukiza pamaso panu,Ndi nsembe yopsereza yamphumphu pa guwa la nsembe lanu.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 33
Onani Deuteronomo 33:10 nkhani