9 Amene anati za atate wace ndi amai wace, Sindinamuone;Sanazindikira abale ace,Sanadziwa ana ace omwe;Popeza anasamalira mau anu, Nasunga cipangano canu.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 33
Onani Deuteronomo 33:9 nkhani