Deuteronomo 4:12 BL92

12 Pamenepo Yehova ananena ndi inu ali pakati pa moto; munamva kunena kwa mau, osaona maonekedwe, koma kunenako.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 4

Onani Deuteronomo 4:12 nkhani