13 Pamenepo anakufotokozerani cipangano cace, cimene anakulamulirani kucicita, ndiwo Mau Khumi; nawalemba pa magome awiri amiyala.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 4
Onani Deuteronomo 4:13 nkhani