1 Ndipo Mose anaitana Israyeli wonse, nanena nao, Tamverani, Israyeli, malemba ndi maweruzo ndinenawa m'makutu mwanu lero, kuti muwaphunzire, ndi kusamalira kuwacita.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 5
Onani Deuteronomo 5:1 nkhani