29 Ha! mwenzi akadakhala nao mtima wotere wakundiopa Ine, ndi kusunga malamulo anga masiku onse, kuti ciwakomere iwo ndi ana ao nthawi zonse!
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 5
Onani Deuteronomo 5:29 nkhani