33 Muziyenda m'njira yonse imene Yehova Mulungu wanu anakulamulirani, kuti mukakhale ndi moyo, ndi kuti cikukomereni, ndi kuti masiku anu acuruke m'dziko limene mudzakhala nalo lanu lanu.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 5
Onani Deuteronomo 5:33 nkhani