8 Usadzipangire iwe wekha fano losema, kapena cifaniziro ciri conse ca zinthu za m'thambo la kumwamba, kapena za m'dziko lapansi, kapena za m'madzi a pansi pa dziko;
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 5
Onani Deuteronomo 5:8 nkhani