2 kuti muope Yehova Mulungu wanu, kusunga malemba ace onse ndi malamulo ace, amene ndikuuzani inu ndi ana anu, ndi zidzukulu zanu, masiku onse a moyo wanu, ndi kuti masiku anu acuruke.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 6
Onani Deuteronomo 6:2 nkhani