Deuteronomo 6:3 BL92

3 Potero imvani, Israyeli, musamalire kuwacita, kuti cikukomereni ndi kuti mucuruke cicurukire, monga Yehova Mulungu wa makolo anu anena ndi inu, m'dziko moyenda mkaka ndi uci ngati madzi.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 6

Onani Deuteronomo 6:3 nkhani