Deuteronomo 7:14 BL92

14 Mudzakhala odalitsika koposa mitundu yonse ya anthu; sipadzakhala mwamuna kapena wamkazi wosabala pakati pa inu, kapena pakati pa zoweta zanu.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 7

Onani Deuteronomo 7:14 nkhani