15 Ndipo Yehova adzakucotserani nthenda zonse; sadzakuikirani nthenda zoipa ziri zonse za Aigupto muzidziwa zija; koma adzaziika pa onse akudana ndi inu.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 7
Onani Deuteronomo 7:15 nkhani