15 amene anakutsogolerani m'cipululu cacikuru ndi coopsaco, munali njoka zamoto, ndi zinkhanira, mouma mopanda madzi; amene anakuturutsirani madzi m'thanthwe lansangalabwi;
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 8
Onani Deuteronomo 8:15 nkhani