16 amene anakudyetsani m'cipululu ndi mana, amene makolo anu sanawadziwa; kuti akucepetseni, ndi kuti akuyeseni, kuti akucitireni cokoma potsiriza panu;
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 8
Onani Deuteronomo 8:16 nkhani