18 Koma mukumbukile Yehova Mulungu wanu, popeza ndi Iyeyu wakupatsani mphamvu yakuonera cuma; kuti akhazikitse cipangano cace cimene analumbirira makolo anu, monga cikhala lero lino.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 8
Onani Deuteronomo 8:18 nkhani