19 Ndipo kudzakhala kuti mukaiwalatu Yehova Mulungu wanu, ndi kutsata milungu yina ndi kuitumikira, ndikucitirani mboni lero lino kuti mudzaonongeka ndithu.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 8
Onani Deuteronomo 8:19 nkhani