15 Kuli konse anaturuka, dzanja la Yehova linawakhalira moipa, monga Yehova adanena, ndi monga Yehova adawalumbirira; nasautsika kwambiri iwowa.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 2
Onani Oweruza 2:15 nkhani