Oweruza 9:24 BL92

24 kuti ciwawa adacitira ana amuna makumi asanu ndi awiria Yerubaala cimdzere, ndi kuti mwazi wao uikidwe pa mbale wao Abimeleki anawaphayo, ndi pa eni ace a ku Sekemu, amene analimbikitsa manja ace, awaphe abale ace.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 9

Onani Oweruza 9:24 nkhani