Yoswa 1:13 BL92

13 Kumbukilani mau amene Mose mtumiki wa Yehova anakulamulirani inu, kuti, Yehova Mulungu wanu akupatsani mpumulo, nadzakupatsani dziko lino.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 1

Onani Yoswa 1:13 nkhani