Yoswa 1:16 BL92

16 Ndipo anamyankha Yoswa, nati, Zonse mwatilamulira tidzacita, ndipo kuli konse mutitumako tidzamuka.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 1

Onani Yoswa 1:16 nkhani