9 Kodi sindinakulamulira iwe? Khala wamphamvu, nulimbike mtima, usaope, kapena kutenga nkhawa, pakuti Yehova Mulungu wako ali ndi iwe kuli konse umukako.
Werengani mutu wathunthu Yoswa 1
Onani Yoswa 1:9 nkhani