Yoswa 10:10 BL92

10 Ndipo Yehova anawamwaza pamaso pa Israyeli, ndipo anawakantha makanthidwe akuru ku Gibeoni, nawapitikitsa pa njira yokwera ya Betihoroni, nawakantha mpaka Azeka, ndi mpaka Makeda.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 10

Onani Yoswa 10:10 nkhani