10 Ndipo Yoswa anabwerera m'mbuyo nthawi imeneyi nalanda Hazori nakantha mfumu yace ndi lupanga; pakuti kale Hazori unali waukuru wa maufumu aja onse.
Werengani mutu wathunthu Yoswa 11
Onani Yoswa 11:10 nkhani