Yoswa 11:23 BL92

23 Motero Yoswa analanda dziko lonse monga mwa zonse Yehova adazinena kwa Mose; ndipo Yoswa analipereka kwa Israyeli, likhale lao lao, pfuko liri lonse gawo lace. Ndipo dziko linapumula nkhondo.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 11

Onani Yoswa 11:23 nkhani