4 Ndipo anaturuka, iwo ndi makamu ao onse nao, anthu ambiri, kucuruka kwao ngati mcenga uli m'mphepete mwa nyanja; ndi akavalo ndi magareta ambirimbiri.
Werengani mutu wathunthu Yoswa 11
Onani Yoswa 11:4 nkhani