23 Ndipo malire a ana a Rubeni ndiwo Yordano ndi malire ace. Ndico colandira ca ana a Rubeni monga mwa mabanja ao, midzi yace ndi miraga yace.
Werengani mutu wathunthu Yoswa 13
Onani Yoswa 13:23 nkhani