Yoswa 15:21 BL92

21 Ndipo midzi ya ku malekezero a pfuko la ana a Yuda ku malire a Edomu, kumwela ndiwo, Kabizeeli ndi Ederi, ndi Yaguri;

Werengani mutu wathunthu Yoswa 15

Onani Yoswa 15:21 nkhani