10 Ndipo a sanaingitsa Akanani akukhala m'Gezeri; koma Akanani anakhala pakati pa Efraimu, kufikira lero lino, nawasonkhera msonkho.
Werengani mutu wathunthu Yoswa 16
Onani Yoswa 16:10 nkhani