8 Kuyambira ku Tapua malire anamuka kumadzulo ku mtsinje wa Kana; ndi maturukiro ace anali kunyanja. Ici ndi colowa ca pfuko la ana a Efraimu monga mwa mabanja ao;
Werengani mutu wathunthu Yoswa 16
Onani Yoswa 16:8 nkhani