Yoswa 17:6 BL92

6 popeza ana akazi a Manase adalandira colowa pakati pa ana ace amuna; ndi dziko la Gileadi linakhala la ana a Manase otsala.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 17

Onani Yoswa 17:6 nkhani