4 Mudzifunire amuna, pfuko liri lonse amuna atatu; kuti ndiwatume, anyamuke, nayendeyende iwo pakati pa dziko, nalilembe monga mwa colowa cao; nabwereoso kwa ine.
Werengani mutu wathunthu Yoswa 18
Onani Yoswa 18:4 nkhani