10 Ndipo maere acitatu anakwecera ana a Zebuloni monga mwa mabanja ao; ndi malire a colowa cao anafikira ku Saridi;
Werengani mutu wathunthu Yoswa 19
Onani Yoswa 19:10 nkhani