Yoswa 2:11 BL92

11 Ndipo titamva ici mitima yathu inasungunuka; anahbenso mtima ndi mmodzi yense, cifukwa ca inu; pakuti Yehova Mulungu wanu, ndiye Mulungu wa m'mwamba umo, ndi pa dziko lapansi.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 2

Onani Yoswa 2:11 nkhani