Yoswa 2:16 BL92

16 Ndipo anati kwa iwo, Mukani kuphiri, olondola angakupezeni; mubisale kumeneko masiku atatu, mpaka atabwerera olondolawo, pamenepo muyende ulendo wanu.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 2

Onani Yoswa 2:16 nkhani