Yoswa 2:7 BL92

7 Ndipo amunawo anawalondola pa njira ya ku Yordano yomka kudooko; ndipo ataturuka akuwalondola, anatseka pacipata.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 2

Onani Yoswa 2:7 nkhani