Yoswa 2:9 BL92

9 nati kwa amunawo, Ndidziwa kuti Yehova wakupatsani dzikoli, ndi kuti kuopsa kwanu kwatigwera, ndi kuti okhala m'dziko onse asungunuka pamaso panu.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 2

Onani Yoswa 2:9 nkhani