Yoswa 20:5 BL92

5 Ndipo akamlondola wolipsa mwazi, asampereke m'dzanja lace wakupha mnzaceyo; pakuti anakantha mnansi wace mosadziwa, osamuda kale.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 20

Onani Yoswa 20:5 nkhani