7 Ndipo anapatula Kedesi m'Galileya ku mapiri a Nafitali, ndi Sekemu ku mapiri a Efraimu, ndi mudzi wa Ariba ndiwo Hebroni ku mapiri a Yuda.
Werengani mutu wathunthu Yoswa 20
Onani Yoswa 20:7 nkhani