5 Ndipo ana otsala a Kohati analandira molota maere motapa pa mabanja a pfuko la Efraimu, ndi pa pfuko La Dani, ndi pa pfuko La Manase logawika pakati, midzi khumi.
Werengani mutu wathunthu Yoswa 21
Onani Yoswa 21:5 nkhani