20 Kodi Akani mwana wa Zera sanalakwa m'coperekedwaco, ndipo mkwiyo unagwera msonkhano wonse wa Israyeli? osangoonongeka yekha munthuyo mu mphulupulu yace.
Werengani mutu wathunthu Yoswa 22
Onani Yoswa 22:20 nkhani