10 Munthu mmodzi wa inu adzapitikitsa anthu cikwi cimodzi; pakuti Yehova Mulungu wanu ndiye amathirira inu nkhondo monga ananena ndi inu.
Werengani mutu wathunthu Yoswa 23
Onani Yoswa 23:10 nkhani