3 ndipo munapenya zonse Yehova Mulungu anacitira mitundu iyi yonse ya anthu cifukwa ca inu; pakuti Yehova Mulungu wanu ndiye anakuthirirani nkhondo.
Werengani mutu wathunthu Yoswa 23
Onani Yoswa 23:3 nkhani