Yoswa 24:31 BL92

31 Ndipo Israyeli anatumikira Yehova masiku onse a Yoswa, ndi masiku onse a akulu akulu otsala atafa Yoswa, amene anadziwa nchito yonse ya Yehova anaicitira Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 24

Onani Yoswa 24:31 nkhani